["Yehova, mtima wanga sunadzikuzendi maso anga sanakwezeke;ndipo sindinatsate zazikulu,kapena zodabwitsa zondiposa.","Indedi, ndinalinganiza ndi kutontholetsa moyo wanga;ngati mwana womletsa kuyamwa amake,moyo wanga ndili nao ngati mwana womletsa kuyamwa.","Israele, uyembekezere Yehova,kuyambira tsopano kufikira kosatha."]